Psalms 140:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amanola lilime lao kuti likhale ngati la njoka, m'kamwa mwao muli ululu wa mamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anola lilime lao ngati njoka; pansi pa milomo yao pali ululu wa mphiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amanola malilime awo kukhala akuthwa ngati a njoka; pa milomo yawo pali ululu wa mamba. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anola lilime lao ngati njoka; Pansi pa milomo yao pali ululu wa mphiri.