Psalms 140:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, tetezeni kwa anthu oipa, tchinjirizeni kwa anthu andeu, amene amaganiza zofuna kundigwetsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndilindireni Yehova, ndisalowe m'manja mwa woipa; ndisungeni kwa munthu wachiwawa; kwa iwo akuti akankhe mapazi anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tetezeni Inu Yehova, kwa anthu oyipa; tchinjirizeni kwa anthu ankhanza amene amakonza zokola mapazi anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndilindireni Yehova, ndisalowe m'manja mwa woipa; Ndisungeni kwa munthu waciwawa; Kwa iwo akuti akankhe mapazi anga.