Psalms 140:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimauza Chauta kuti, “Inu ndinu Mulungu wanga,” tcherani khutu kuti mumve liwu la kupemba kwanga, Inu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinati kwa Yehova, Inu ndinu Mulungu wanga; munditcherere khutu mau a kupemba kwanga, Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova, ine ndikuti, “Ndinu Mulungu wanga.” Imvani kupempha kwanga Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinati kwa Yehova, Inu ndinu Mulungu wanga; Mundicherere khutu mau a kupemba kwanga, Yehova.