Psalms 141:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pemphero langa likwere kwa Inu ngati lubani, kukweza kwa manja anga kukhale ngati nsembe yamadzulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pemphero langa liikike ngati chofukiza pamaso panu; kukweza manja anga kuikike ngati nsembe ya madzulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pemphero langa lifike kwa Inu ngati lubani; kukweza manja kwanga kukhale ngati nsembe yamadzulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pempherolanga liikike ngaticofukiza pamaso panu; Kukweza manja anga kuikike ngati nsembe ya madzulo.