Psalms 141:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu oipa akadzaperekedwa kwa oŵalanga, pamenepo adzaphunzira kuti mau a Chauta ndi oona.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Oweruza ao anagwetseka pambali pa thanthwe; nadzamva mau anga kuti ndiwo okondweretsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Olamulira awo adzaponyedwa pansi kuchokera pa malo okwera kwambiri, ndipo anthu oyipa adzaphunzira kuti mawu anga anayankhulidwa bwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Oweruza ao anagwetseka pambali pa thanthwe; Nadzamva mau anga kuti ndiwo okondweretsa.