Psalms 141:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga momwe nkhuni zimamwazikira akaziŵaza, ndi m'menenso mafupa ao adzamwazikira ku manda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mafupa athu amwazika pakamwa pa manda, monga ngati akumba nanyimphula nthaka yapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo adzati, “Monga momwe nkhuni zimamwazikira akaziwaza, ndi momwenso mafupa athu amwazikira pa khomo la manda.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mafupa athu amwazika pakamwa pa manda, Monga ngati akumba nanyimphula nthaka yapansi.