Psalms 141:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma maso anga amayang'anirabe kwa Inu, Chauta Mulungu wanga. Ndimathaŵira kwa Inu kuti munditeteze, musandisiye opanda wonditchinjiriza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti maso anga apenya kwanu, Yehova Ambuye; ndithawira kwa Inu; musataye moyo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma maso anga akupenyetsetsa Inu Ambuye Wamphamvuzonse; ndimathawira kwa Inu, musandipereke ku imfa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti maso anga apenya kwanu, Yehova Ambuye; Ndithawira kwa Inu; musataye moyowanga.