Psalms 142:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikupereka madandaulo anga kwa Iye, ndikutchula mavuto anga pamaso pake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nditsanulira kudandaula kwanga pamaso pake; ndionetsa msauko wanga pamaso pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikukhuthula madandawulo anga pamaso pake; ndikufotokoza za masautso anga pamaso pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nditsanulirakudandaulakwanga pamaso pace; Ndionetsa msauko wanga pamaso pace.