Psalms 142:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikayang'ana ku dzanja lamanja, palibe ndi mmodzi yemwe wosamalako za ine. Kulibe koti ndithaŵire, palibe munthu wondisamala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Penyani kudzanja lamanja ndipo muone; palibe wondidziwa; pothawirapo pandisowa; palibe mmodzi wosamalira moyo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yangʼanani kumanja kwanga ndipo onani; palibe amene akukhudzika nane. Ndilibe pothawira; palibe amene amasamala za moyo wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Penyani ku dzanja lamanja ndipo muone; palibe wondidziwa; Pothawirapo pandisowa; palibe mmodzi wosamalira moyo wanga.