Psalms 142:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimalirira Inu Chauta, ndimati, “Inu ndinu kothaŵira kwanga, ndinu zanga zonse m'dziko la amoyo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinafuulira kwa inu, Yehova; ndinati, Inu ndinu pothawirapo panga, gawo langa m'dziko la amoyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndilirira Inu Yehova; ndikuti, “Ndinu pothawirapo panga, gawo langa mʼdziko la anthu amoyo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinapfuulira kwa inu, Yehova; Ndina, Inu ndinu pothawirapo panga, Gawo langa m'dziko la amoyo.