Psalms 142:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imvani kulira kwanga, pakuti ndataya mtima. Pulumutseni kwa ondizunza, chifukwa andiposa mphamvu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tamverani kufuula kwanga; popeza ndisauka kwambiri; ndilanditseni kwa iwo akundilondola; popeza andilaka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mverani kulira kwanga pakuti ndathedwa nzeru; pulumutseni kwa amene akundithamangitsa pakuti ndi amphamvu kuposa ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tamverani kupfuula kwanga; papeza ndisauka kwambiri; Ndilanditseni kwa iwo akundilondola; popeza andilaka.