Psalms 142:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tulutseni m'ndende kuti ndizitamanda dzina lanu. Anthu anu adzandizungulira, chifukwa Inu mwandichitira zabwino zambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tulutsani moyo wanga m'ndende, kuti ndiyamike dzina lanu; olungama adzandizinga; pakuti mudzandichitira zokoma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tulutseni mʼndende yanga kuti nditamande dzina lanu. Ndipo anthu olungama adzandizungulira chifukwa cha zabwino zanu pa ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Turutsani moyo wanga m'ndende, kuti ndiyamike dzina lanu; Olungama adzandizinga; Pakuti mudzandicitira zokoma.