Psalms 143:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sungani moyo wanga, Inu Chauta, kuti dzina lanu lilemekezeke. Munditulutse pa mavuto chifukwa cha kulungama kwanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundipatse moyo, Yehova, chifukwa cha dzina lanu; mwa chilungamo chanu mutulutse moyo wanga m'sautso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sungani moyo wanga Inu Yehova chifukwa cha dzina lanu; mwa chilungamo chanu tulutseni mʼmasautso anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundipatse moyo, Yehova, cifukwa ca dzina lanu; Mwa cilungamo canu muturutse moyo wanga m'nsautso.