Psalms 143:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kanthani adani anga chifukwa cha chikondi chanu chosasinthika pa ine. Muwononge onse ondizunza, pakuti ine ndine mtumiki wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mwa chifundo chanu mundidulire adani anga, ndipo muononge onse akusautsa moyo wanga; pakuti ine ndine mtumiki wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwa chikondi chanu chosasinthika khalitsani chete adani anga; wonongani adani anga, pakuti ndine mtumiki wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mwa cifundo canu mundidulire adani anga, Ndipo muononge onse akusautsa moyo wanga; Pakuti ine ndine mtumiki wanu.