Psalms 143:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musandizenge mlandu ine mtumiki wanu, popeza kuti palibe munthu wamoyo amene ali wolungama pamaso panu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo musaitane mlandu wa mtumiki wanu; pakuti pamaso panu sipadzakhala wolungama wamoyo mmodzi yense.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musazenge mlandu mtumiki wanu, pakuti palibe munthu wamoyo amene ndi wolungama pamaso panu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo musaitane mlandu wa mtumiki wanu; Pakuti pamaso panu sipadzakhala wolungama wamoyo mmodzi yense.