Psalms 143:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mdani wandilondola, wavimviniza moyo wanga m'dothi, wandikhazika mu mdima, ngati anthu amene adafa kale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mdani alondola moyo wanga; apondereza pansi moyo wanga; andikhalitsa mumdima monga iwo adafa kale lomwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mdani akundithamangitsa, iye wandipondereza pansi; wachititsa kuti ndikhale mu mdima ngati munthu amene anafa kale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mdani alondola moyo wanga; Apondereza pansr moyo wanga; Andikhalitsa mumdima monga iwo adafa kale lomwe.