Psalms 143:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake mtima wanga wafooka m'kati mwanga, mumtima mwangamu mukuchita mantha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero mzimu wanga wakomoka mwa ine; mtima wanga utenga nkhawa m'kati mwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho mzimu wanga ukufowoka mʼkati mwanga; mʼkati mwanga, mtima wanga uli ndi nkhawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero mzimu wanga wakomoka mwa ine; Mtima wanga utenga nkhawa m'kati mwanga,