Psalms 143:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimakumbukira masiku amakedzana, ndimasinkhasinkha za zonse zimene mwazichita, ndimalingalira ntchito za manja anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikumbukira masiku a kale lomwe; zija mudazichita ndilingirirapo; ndikamba pandekha za ntchito ya manja anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndimakumbukira masiku amakedzana; ndimalingalira za ntchito yanu yonse, ndimaganizira zimene manja anu anachita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikumbukila masiku a kale lomwe; Zija mudazicita ndilingirirapo; Ndikamba pa ndekha za nchito ya manja anu.