Psalms 143:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, pulumutseni kwa adani anga, chifukwa ndathaŵira kwa Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundilanditse kwa adani anga, Yehova; ndibisala mwa Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pulumutseni kwa adani anga, Inu Yehova, pakuti ndimabisala mwa Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundilanditse kwa adani anga, Yehova; Ndibisala mwa Inu.