Psalms 144:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atamandike Chauta, thanthwe langa londitchinjiriza, amene amaphunzitsa manja anga ndi zala zanga kumenya nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Salimo la Davide. Wolemekezeka Yehova thanthwe langa, wakuphunzitsa manja anga achite nkhondo, zala zanga zigwirane nao:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo la Davide. Atamandike Yehova Thanthwe langa, amene amaphunzitsa manja anga kuchita nkhondo; zala zanga kumenya nkhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wolemekezeka Yehova thanthwe langa, Wakuphunzitsa manja anga acite nkhondo, Zala zanga zigwirane nao: