Psalms 144:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Landitseni kwa adani ankhalwe, mundipulumutse m'manja mwa akunja, amene amalankhula zabodza, ndipo amalumbira zonama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndilanditseni ndi kundipulumutsa kudzanja la alendo, amene pakamwa pao alankhula zachabe, ndi dzanja lao lamanja ndilo dzanja lachinyengo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Landitseni ndi kundipulumutsa, mʼmanja mwa anthu achilendo, amene pakamwa pawo ndi podzaza ndi mabodza, amene dzanja lawo lamanja ndi lachinyengo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndilanditseni ndi kundipulumutsa ku dzanja la alendo, Amene pakamwa pao alankhula zacabe, Ndi dzanja lao lamanja ndilo dzanja lacinyengo.