Psalms 144:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ng'ombe zathu zikhale ndi maŵele, zisapoloze kapena kulephera kubereka. M'miseu mwathu musakhale kulira chifukwa cha mavuto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuti ng'ombe zathu zikhale zosenza katundu; ndi kuti pasakhale kupasula linga kapena kutulukamo, pasakhalenso kufuula m'makwalala athu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngʼombe zathu zidzanyamula katundu wolemera. Sipadzakhala mingʼalu pa makoma, sipadzakhalanso kupita ku ukapolo, mʼmisewu mwathu simudzakhala kulira chifukwa cha mavuto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti ng'ombe zathu zikhale zasenza katundu; Ndi kuti pasakhale kupasula linga kapena kuturukamo, Pasakhalenso kupfuula m'makwalala athu.