Psalms 144:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngodala anthu olandira madalitso ameneŵa. Ngodala anthu amene Mulungu wao ndi Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Odala anthu akuona zotere; odala anthu amene Mulungu wao ndi Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Odala anthu amene adzalandira madalitso awa; odala anthu amene Mulungu wawo ndi Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Odala anthu akuona zotere; Odala anthu amene Mulungu wao ndi Yehova.