Psalms 144:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, kodi munthu nchiyani, kuti muzimsamala? Mwana wa munthu nchiyani, kuti muzimganizira?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova, munthu ndani kuti mumdziwa? Mwana wa munthu kuti mumsamalira?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova, munthu nʼchiyani kuti mumamusamalira, mwana wa munthu kuti muzimuganizira?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova, munthu ndani kuti mumdziwa? Mwana wa munthu kuti mumsamalira?