Psalms 144:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu ali ngati mpweya, masiku ake ali ngati mthunzi wosakhalitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu akunga mpweya; masiku ake akunga mthunzi wopitirira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu ali ngati mpweya; masiku ake ali ngati mthunzi wosakhalitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu akunga mpweya; Masiku ace akunga mthunzi wopitirira.