Psalms 144:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ng'animitsani zing'aning'ani ndi kuŵamwaza adani anga. Ponyani mivi yanu, ndi kuŵapirikitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ng'animitsani mphezi, ndi kuwabalalitsa; tumizani mivi yanu, ndi kuwapirikitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tumizani zingʼaningʼani ndi kubalalitsa adani; ponyani mivi yanu ndi kuwathamangitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ng'animitsani mphezi, ndi kuwabalalitsa; Tumizani mibvi yanu, ndi kuwapitikitsa,