Psalms 144:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tambasulani dzanja lanu kuchokera kumwamba. Landitseni ndi kundipulumutsa ku madzi ozama, omboleni m'manja mwa akunja,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tulutsani manja anu kuchokera m'mwamba; ndikwatuleni ndi kundilanditsa kumadzi aakulu, kudzanja la alendo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tambasulani dzanja lanu kuchokera kumwamba; landitseni ndi kundipulumutsa, ku madzi amphamvu, mʼmanja mwa anthu achilendo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Turutsani manja anu kucokera m'mwamba; Ndikwatuleni ndi kundilanditsa ku madzi akuru, Ku dzanja la alendo;