Psalms 144:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakuimbirani nyimbo yatsopano, Inu Mulungu. Ndidzakuimbirani zeze wa nsambo khumi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzakuimbirani nyimbo yatsopano, Mulungu; pa chisakasa cha zingwe khumi ndidzaimbira zakukulemekezani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakuyimbirani nyimbo yatsopano Inu Mulungu; ndidzakuyimbirani nyimbo pa zeze wa nsambo khumi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzakuyimbirani nyimbo yatsopano, Mulungu; Pa cisakasa ca zingwe khumi ndidzayimbira zakukulemekezani.