Psalms 145:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakuyamikani, Inu Mulungu wanga, mfumu yanga, ndidzalemekeza dzina lanu nthaŵi zonse mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Salimo lolemekeza; la Davide. Ndidzakukwezani Mulungu wanga, Mfumu; ndipo ndidzalemekeza dzina lanu kunthawi za nthawi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo la matamando la Davide. Ndidzakukwezani Mulungu wanga, Mfumu yanga; ndidzatamanda dzina lanu ku nthawi za nthawi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzakukwezani Mulungu wanga, Mfumu; Ndipo ndidzalemekeza dzina lanu ku nthawi za nthawi.