Psalms 145:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zamoyo zonse zidzakuthokozani, Inu Chauta, anthu anu onse oyera mtima adzakutamandani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ntchito zanu zonse zidzakuyamikani, Yehova; ndi okondedwa anu adzakulemekezani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zonse zimene munazipanga zidzakutamandani, Inu Yehova; oyera mtima adzakulemekezani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nchito zanu zonse zidzakuyamikani, Yehova; Ndi okondedwa anu adzakulemekezani.