Psalms 145:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzalankhula za ulemerero wa ufumu wanu, adzasimba za mphamvu zanu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzanenera ulemerero wa ufumu wanu, adzalankhulira mphamvu yanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo adzafotokoza za ulemerero wa ufumu wanu ndi kuyankhula za mphamvu yanu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzanenera ulemerero wa ufumu wanu, Adzalankhulira mphamvu yanu;