Psalms 145:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti adziŵitse anthu onse za ntchito zanu zamphamvu, kutinso asimbe za ulemerero ndi za ufumu wanu waukulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kudziwitsa ana a anthu zamphamvu zake, ndi ulemerero waukulu wa ufumu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti anthu onse adziwe za machitidwe anu amphamvu ndi ulemerero wokongola wa ufumu wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kudziwitsa ana a anthu zamphamvu zace, Ndi ulemerero waukuru wa ufumu wace.