Psalms 145:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ufumu wanu ndi ufumu wamuyaya, ulamuliro wanu ndi wa pa mibadwo yonse. Chauta ndi wokhulupirika pa mau ake onse, ndi wokoma mtima pa zochita zake zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ufumu wanu ndiwo ufumu womka muyaya, ndi kuweruza kwanu kufikira mibadwo yonseyonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ufumu wanu ndi ufumu wamuyaya, ndipo ulamuliro wanu ndi wosatha pa mibado yonse. Yehova ndi wokhulupirika pa malonjezo ake onse ndi wokonda zonse zimene Iye anazipanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ufumu wanu ndiwo ufumu womka muyaya, Ndi kuweruza kwanu kufikira mibadwo yonse yonse.