Psalms 145:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene amamvera Chauta, amaŵapatsa zofuna zao, amamvanso kulira kwao, naŵapulumutsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzachita chokhumba iwo akumuopa; nadzamva kufuula kwao, nadzawapulumutsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amakwaniritsa zokhumba za iwo amene amamuopa; amamva kulira kwawo ndi kuwapulumutsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzacita cokhumba iwo akumuopa; Nadzamva kupfuula kwao, nadzawapulumutsa.