Psalms 145:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakuthokozani tsiku ndi tsiku, ndidzatamanda dzina lanu mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku onse ndidzakuyamikani; ndi kulemekeza dzina lanu kunthawi za nthawi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakutamandani tsiku ndi tsiku ndi kulemekeza dzina lanu ku nthawi za nthawi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku onse ndidzakuyamikani; Ndi kulemekeza dzina lanu ku nthawi za nthawi.