Psalms 145:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu adzasimba za mphamvu zanu zoopsa, inenso ndidzalalika za ukulu wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzanenera mphamvu za ntchito zanu zoopsa; ndi ukulu wanu ndidzaufotokozera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo adzafotokoza za mphamvu ya ntchito zanu zoopsa kwambiri, ndipo ine ndidzalengeza za ntchito zanu zazikulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzanenera mphamvu za nchito zanu zoopsa; Ndi ukulu wanu ndidzaufotokozera.