Psalms 145:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ndi wokoma mtima ndi wachifundo, wosakwiya msanga, wodzaza ndi chikondi chosasinthika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova ndiye wachisomo, ndi wachifundo; osakwiya msanga, ndi wa chifundo chachikulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova ndi wokoma mtima ndi wachifundo, wosakwiya msanga ndi wodzaza ndi chikondi chosasinthika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova ndiye wacisomo, ndi wacifundo; Osakwiya msanga, ndi wa cifundo cacikuru.