Psalms 146:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adzakhala mfumu mpaka muyaya, Mulungu wako, iwe Ziyoni, adzalamulira ku mibadwo yonse. Tamandani Chauta!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova adzachita ufumu kosatha, Mulungu wako, Ziyoni, ku mibadwomibadwo. Aleluya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova ndiye Mfumu mpaka muyaya, Mulungu wako iwe Ziyoni, pa mibado yonse. Tamandani Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova adzacita ufumu kosatha, Mulungu wako, Ziyoni, ku mibadwo mibadwo. Haleluya.