Psalms 146:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adalenga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zimene zili m'menemo. Amasunga malonjezo ake nthaŵi zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amene analenga zakumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zili m'mwemo. Ndiye wakusunga choonadi kosatha,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wolenga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zili mʼmenemo; Yehova, amene ndi wokhulupirika kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene analenga zakumwamba ndi dziko lapansi, Nyanja ndi zonse ziri m'mwemo; Ndiye wakusunga coonadi kosatha: