Psalms 146:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amachitira anthu opsinjidwa zolungama, amaŵapatsa chakudya anthu anjala. Chauta amamasula am'ndende.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndiye wakuchitira chiweruzo osautsika; ndiye wakupatsa anjala chakudya; Yehova amasula akaidi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amachitira chilungamo anthu oponderezedwa ndipo amapereka chakudya kwa anthu anjala. Yehova amamasula amʼndende,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiye wakucitira ciweruzo osautsika; Ndiye wakupatsa anjala cakudya; Yehova amasula akaidi;