Psalms 147:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tamandani Chauta! Nkwabwino kuimba nyimbo zotamanda Mulungu wathu, nkokondwetsa mtima kumtamanda moyenera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aleluya; Pakuti kuimbira zomlemekeza Mulungu wathu nkokoma; pakuti chikondwetsa ichi, chilemekezo chiyenera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tamandani Yehova. Nʼkwabwino kwambiri kuyimba nyimbo zamatamando kwa Mulungu wathu, nʼkokondweretsa ndi koyenera kumutamanda!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Haleluya; Pakuti kuyimbira zomlemekeza Mulungu wathu nkokoma; Pakuti cikondwetsa ici, cilemekezo ciyenera.