Psalms 147:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Chauta amakondwera ndi anthu omuwopa, amene amadalira chikondi chake chosasinthika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova akondwera nao akumuopa Iye, iwo akuyembekeza chifundo chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova amakondwera ndi amene amamuopa, amene chiyembekezo chawo chili mʼchikondi chake chosasinthika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova akondwera nao akumuopa Iye, Iwo akuyembekeza cifundo cace.