Psalms 147:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amagwetsa matalala ngati miyala. Kodi ndani angathe kupirira kuzizira kwake?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aponya matalala ake ngati zidutsu: Adzaima ndani pa kuzizira kwake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amagwetsa matalala ngati miyala. Kodi ndani angathe kupirira kuzizira kwake?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aponya matalala ace ngati zidutsu: Adzaima ndani pa kuzizira kwace?