Psalms 147:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sadachitepo zimenezi ndi mtundu wina uliwonse wa anthu, iwo sadziŵa malangizo ake. Tamandani Chauta!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sanatero nao anthu a mtundu wina; ndipo za maweruzo ake, sanawadziwe. Aleluya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sanachitepo zimenezi kwa mtundu wina uliwonse wa anthu; anthu enawo sadziwa malamulo ake. Tamandani Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sanatero nao anthu amtundu wina; Ndipo za maweruzo ace, sanawadziwa. Haleluya.