Psalms 147:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbuye wathu ndi wamkulu, ndipo ndi wa mphamvu zambiri, nzeru zake nzopanda malire.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ambuye wathu ndi wamkulu ndi wa mphamvu zambiri; nzeru yake njosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova ndi wamkulu ndi wamphamvu kwambiri; nzeru zake zilibe malire.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ambuye wathu ndi wamkuru ndi wa mphamvu zambiri; Nzeru yace njosatha.