Psalms 147:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imbirani Chauta mothokoza, imbirani Mulungu wathu nyimbo yokoma ndi pangwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yamikani Yehova ndi kuthira mang'ombe; muimbireni Mulungu wathu zomlemekeza pazeze:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Imbirani Yehova ndi mayamiko; imbani nyimbo kwa Mulungu ndi pangwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yamikani Yehova ndi kuthira mang'ombe; Myimbireni Mulungu wathu zamlemekeza pazeze: