Psalms 147:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amapereka chakudya kwa nyama ndi kwa ana a khungubwi pamene akulira chakudya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amene apatsa zoweta chakudya chao, ana a khungubwi alikulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amapereka chakudya kwa ngʼombe ndi kwa ana a makwangwala pamene akulira chakudya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene apatsa zoweta cakudya cao, Ana a khungubwi alikulira.