Psalms 148:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mafumu a pa dziko lapansi ndi anthu a mitundu yonse, inu akuluakulu ndi olamulira dziko lapansi!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mafumu a padziko ndi mitundu yonse ya anthu; zinduna ndi oweruza onse a padziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mafumu a dziko lapansi ndi anthu a mitundu yonse, inu akalonga ndi olamulira a dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mafumu a padziko ndi mitundu yonse ya anthu; Zinduna ndi oweruza onse a padziko;