Psalms 148:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtamandeni inu thambo lakumwambamwamba, ndi inu madzi a pamwamba pa thambo!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mlemekezeni, m'mwambamwamba, ndi madzi inu, a pamwamba pa thambo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mutamandeni, inu thambo la kumwambamwamba ndi inu madzi a pamwamba pa thambo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mlemekezeni, m'mwambamwamba, Ndi madzi inu, a pamwamba pa thambo.