Psalms 149:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atamande dzina lake povina, amuimbire nyimbo yokoma ndi ng'oma ndi pangwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Alemekeze dzina lake ndi kuthira mang'ombe; amuimbire zomlemekeza ndi lingaka ndi zeze.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atamande dzina lake povina ndi kuyimbira Iye nyimbo ndi tambolini ndi pangwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Alemekeze dzina lace ndi kuthira mang'ombe; Amyimbire zomlemekeza ndi lingaka ndi zeze.